by malawiumc | Dec 14, 2011 | Uncategorized
Wolemba Joseph Kaipa Malawi UMC Communicator Maphuziro abusa omwe anachitikira ku ofesi yaikulu mu mzinda wa Blantyre kuyambira pa 12mpaka pa 16 september 2011 athandiza kusula ophuzirawa kukhala akadaulo pa ntchito imene Mulungu anawapatsa....